
Malawi iphunzire kusamala ndalama, 4 billion Kwacha ikanapulumuka pa ntchito yomanga Commercial court
Maganizo a Malawi24 monga m’mene alilinso a aMalawi ena okhudzidwa, ndi okonda dziko lawo, tikanakonda kuti boma lidzichalira pomanga zitukuko zake zina. Ndi zomvetsa chisoni ndi zowawa kuti ndalama zoposa 4 billion Kwacha zikanatha kupulumuka pa ntchito …